- I.
- Mulungu dalitsa Malaŵi,
- Mumsunge m'mtendere.
- Gonjetsani adani onse,
- Njala, nthenda, nsanje.
- Lunzitsani mitima yathu,
- Kuti tisaope.
- Mdalitse Mtsogo leri nafe,
- Ndi Mayi Malaŵi.
- II.
- Malaŵi ndziko lokongola,
- La chonde ndi ufulu,
- Nyanja ndi mphepo ya m'mapiri,
- Ndithudi tadala.
- Zigwa, mapiri, nthaka, dzinthu,
- N'mphatso zaulere.
- Nkhalango, madambo abwino.
- Ngwokoma Malaŵi.
- III.
- O Ufulu tigwirizane,
- Kukweza Malaŵi.
- Ndi chikondi, khama, kumvera,
- Timutumikire.
- Pa nkhondo nkana pa mtendere,
- Cholinga n'chimodzi.
- Mayi, bambo, tidzipereke,
- Pokweza Malaŵi.
|
- I.
- 上帝保佑我国马拉维,
- 和平之地永垂。
- 打倒敌人不论哪一类:
- 饥饿、疾病、诋毁。
- 团结一心并结伴相随,
- 再无恐惧包围。
- 保佑领袖不论哪一位,
- 以及母亲马拉维。
- II.
- 美丽土地我们马拉维
- 肥沃勇敢自由。
- 她的湖水清凉的山气,
- 我们无比富裕。
- 山谷沃土我们的祖国,
- 赋予人民自由。
- 从森林到广阔的平原,
- 都是美丽马拉维。
- III.
- 永远自由让我们团结,
- 建立起马拉维。
- 我们的爱和热忱忠诚,
- 为马拉维努力。
- 不论是战争还是和平,
- 都会一心一意。
- 你的儿女们无私奉献,
- 都来建设马拉维。
|